| Chichewa | Malankhulidwe ena |
Kanema ya YESU Mwaona makanema (movies) ambiri koma iyi kanema ni yosiana. Ionetsa umoyo wa Ambuye Yesu kristu ndiponso iyi kanema yatha kusintha umoyo wa anthu ambiri-mbiri. Ciyambire pano padziko lapansi, kulibe
kanema yomwe anthu ambiri-mbiri akhala ndi danga yo ona monga kanema ya
Yesu Kristu. |
© 2002 Campus Crusade for Christ International
Last Updated: 28 November, 2001